Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamndandanda wa mayina a atsogoleri a nyumba ya makolo awo, malinga ndi mibadwo yawo,+ panali amuna amphamvu ndi olimba mtima okwanira 20,200.

  • 1 Mbiri 7:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Onsewa anali ana a Aseri, atsogoleri+ a nyumba ya makolo awo, amuna ochita kusankhidwa, amphamvu ndi olimba mtima.+ Iwo anali akuluakulu a atsogoleri, ndipo mndandanda wa mayina awo+ anaugwiritsa ntchito powalemba usilikali, pokonzekera nkhondo. Analipo amuna 26,000.+

  • Ezara 2:59
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Ndiyeno amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri, ndipo sanathe kupereka umboni wotsimikizira kumene anachokera komanso kuti makolo awo+ anali Aisiraeli, ndi awa:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena