Nehemiya 7:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Ndiyeno amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri,+ ndipo sanathe kufotokoza mzere wa makolo awo ndi kumene anachokera, kuti kaya anali ochokera mu Isiraeli kapena ayi, ndi awa:
61 Ndiyeno amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri,+ ndipo sanathe kufotokoza mzere wa makolo awo ndi kumene anachokera, kuti kaya anali ochokera mu Isiraeli kapena ayi, ndi awa: