Ezara 2:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Ndiyeno amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri, ndipo sanathe kupereka umboni wotsimikizira kumene anachokera komanso kuti makolo awo+ anali Aisiraeli, ndi awa:
59 Ndiyeno amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri, ndipo sanathe kupereka umboni wotsimikizira kumene anachokera komanso kuti makolo awo+ anali Aisiraeli, ndi awa: