Ekisodo 32:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Komabe Yehova anauza Mose kuti: “Amene wandichimwirayo ndi amene ndim’fafanize m’buku langa.+ Chivumbulutso 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo wina akachotsa kalikonse pa mawu a mumpukutu wa ulosi umenewu, Mulungu adzachotsa gawo lake pa zolembedwa mumpukutuwu, kutanthauza kuti sadzamulola kudya zipatso za m’mitengo ya moyo,+ ndipo sadzamulola kulowa mumzinda woyerawo.+
19 Ndipo wina akachotsa kalikonse pa mawu a mumpukutu wa ulosi umenewu, Mulungu adzachotsa gawo lake pa zolembedwa mumpukutuwu, kutanthauza kuti sadzamulola kudya zipatso za m’mitengo ya moyo,+ ndipo sadzamulola kulowa mumzinda woyerawo.+