Ezekieli 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndidzachotsa pakati panu anthu ondipandukira ndi ondichimwira.+ Pakuti ndidzawatulutsa m’dziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa m’dziko la Isiraeli,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
38 Ndidzachotsa pakati panu anthu ondipandukira ndi ondichimwira.+ Pakuti ndidzawatulutsa m’dziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa m’dziko la Isiraeli,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+