Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Inu simudzalowa m’dziko limene ndinachita kukweza dzanja langa+ polumbira kuti ndidzakhala nanu mmenemo, kupatula Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+

  • Ezekieli 34:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kwa iwo kuti: “Ndithu ine ndidzapereka chiweruzo pakati pa nkhosa yonenepa ndi nkhosa yowonda.

  • Malaki 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye adzakhala pansi ngati woyenga zitsulo ndiponso ngati woyeretsa siliva.+ Adzayeretsa ana a Levi+ ndipo adzawayeretsa ngati golide+ ndi siliva. Pamene azidzapereka nsembe zawo ngati mphatso, Yehova adzaona kuti nsembe zawozo akuzipereka+ molungama.

  • Mateyu 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena