Yeremiya 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wadzudzula aneneriwo kuti: “Ndiwadyetsa chitsamba chowawaNdipo ndiwapatsa madzi apoizoni kuti amwe.+ Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko wafalikira mʼdziko lonse.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:15 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 9
15 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wadzudzula aneneriwo kuti: “Ndiwadyetsa chitsamba chowawaNdipo ndiwapatsa madzi apoizoni kuti amwe.+ Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko wafalikira mʼdziko lonse.”