Yeremiya 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wa makamu wadzudzula aneneriwo kuti: “Ndiwadyetsa chitsamba chowawa ndipo ndiwamwetsa madzi apoizoni.+ Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko+ wafalikira m’dziko lonse.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:15 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 9
15 Choncho Yehova wa makamu wadzudzula aneneriwo kuti: “Ndiwadyetsa chitsamba chowawa ndipo ndiwamwetsa madzi apoizoni.+ Chifukwa kuchokera mwa aneneri a ku Yerusalemu mpatuko+ wafalikira m’dziko lonse.”