Yeremiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+ Maliro 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+
9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+
16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+