Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Anthu asokonezeka.+ Nsautso ndi zowawa za pobereka zawagwera. Iwo akumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+ Akuyang’anana modabwa. Nkhope zawo zafiira ndi mantha.+

  • Yeremiya 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ine ndamva mawu ngati a mkazi amene akumva ululu. Ndamva ngati kubuula kwa mkazi amene akubereka mwana wake woyamba,+ koma ndi mawu a mwana wamkazi wa Ziyoni amene akupuma movutikira. Iye akutambasula manja ake+ ndi kulira kuti: “Tsoka ine, chifukwa ndatopa ndi anthu amene akufuna kundipha!”+

  • Yeremiya 6:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ife tamva uthenga wa zimenezi. Manja athu angoti lendee!+ Tagwidwa ndi nkhawa ndipo tikumva ululu ngati wa mkazi amene akubereka.+

  • Mika 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Tsopano n’chifukwa chiyani ukufuula kwambiri?+ Kodi mwa iwe mulibe mfumu, kapena kodi alangizi ako awonongedwa? Kodi n’chifukwa chake zowawa ngati za mkazi amene akubereka zakugwira?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena