Salimo 48:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumeneko iwo anayamba kunjenjemera,+Anamva zopweteka ngati za mkazi amene akubereka.+ Yesaya 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 N’chifukwa chake m’chiuno mwanga mwadzaza ululu woopsa.+ Zopweteka zandigwira, ngati zowawa za mkazi amene akubereka.+ Ndazunguzika moti sindikumva. Ndasokonezeka moti sindikuona. Yeremiya 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+
3 N’chifukwa chake m’chiuno mwanga mwadzaza ululu woopsa.+ Zopweteka zandigwira, ngati zowawa za mkazi amene akubereka.+ Ndazunguzika moti sindikumva. Ndasokonezeka moti sindikuona.
6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+