Ekisodo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+ Yesaya 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu asokonezeka.+ Nsautso ndi zowawa za pobereka zawagwera. Iwo akumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+ Akuyang’anana modabwa. Nkhope zawo zafiira ndi mantha.+ Danieli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi imeneyo nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo inachita mantha.+ Miyendo yake inafooka+ ndipo mawondo ake anayamba kunjenjemera.+
15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+
8 Anthu asokonezeka.+ Nsautso ndi zowawa za pobereka zawagwera. Iwo akumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+ Akuyang’anana modabwa. Nkhope zawo zafiira ndi mantha.+
6 Pa nthawi imeneyo nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo inachita mantha.+ Miyendo yake inafooka+ ndipo mawondo ake anayamba kunjenjemera.+