Yeremiya 50:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Mfumu ya Babulo yamva za iwo,+ ndipo yataya mtima ndi kulefuka.+ Ikuda nkhawa ndipo ikumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+
43 “Mfumu ya Babulo yamva za iwo,+ ndipo yataya mtima ndi kulefuka.+ Ikuda nkhawa ndipo ikumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+