Danieli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi imeneyo nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo inachita mantha.+ Miyendo yake inafooka+ ndipo mawondo ake anayamba kunjenjemera.+
6 Pa nthawi imeneyo nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo inachita mantha.+ Miyendo yake inafooka+ ndipo mawondo ake anayamba kunjenjemera.+