Yeremiya 51:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Munthu mmodzi wothamanga wakumana ndi mnzake, ndipo mthenga mmodzi wakumana ndi mnzake,+ onsewa akukanena kwa mfumu ya Babulo kuti mzinda wake walandidwa kumbali zonse.+
31 “Munthu mmodzi wothamanga wakumana ndi mnzake, ndipo mthenga mmodzi wakumana ndi mnzake,+ onsewa akukanena kwa mfumu ya Babulo kuti mzinda wake walandidwa kumbali zonse.+