Yesaya 47:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsoka lidzakugwera ndipo sudzatha kuliletsa ndi matsenga ako. Mavuto adzakugwera+ ndipo sudzatha kuwapewa. Chiwonongeko chimene sunali kuchiyembekezera chidzakupeza modzidzimutsa.+ Yeremiya 50:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwe Babulo ndinakutchera msampha ndipo wakodwa koma iwe sunadziwe.+ Unapezeka ndi kugwidwa chifukwa unali kulimbana ndi Yehova.+ Yeremiya 50:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Mfumu ya Babulo yamva za iwo,+ ndipo yataya mtima ndi kulefuka.+ Ikuda nkhawa ndipo ikumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+
11 Koma tsoka lidzakugwera ndipo sudzatha kuliletsa ndi matsenga ako. Mavuto adzakugwera+ ndipo sudzatha kuwapewa. Chiwonongeko chimene sunali kuchiyembekezera chidzakupeza modzidzimutsa.+
24 Iwe Babulo ndinakutchera msampha ndipo wakodwa koma iwe sunadziwe.+ Unapezeka ndi kugwidwa chifukwa unali kulimbana ndi Yehova.+
43 “Mfumu ya Babulo yamva za iwo,+ ndipo yataya mtima ndi kulefuka.+ Ikuda nkhawa ndipo ikumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+