Yeremiya 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+ Hoseya 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zowawa ngati za mkazi amene akubereka zidzamugwera.+ Iye ndi mwana wopanda nzeru+ chifukwa nthawi yoti abadwe ikakwana, sadzadziika pamalo amene ana amatulukira pochokera m’chiberekero.+
6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+
13 Zowawa ngati za mkazi amene akubereka zidzamugwera.+ Iye ndi mwana wopanda nzeru+ chifukwa nthawi yoti abadwe ikakwana, sadzadziika pamalo amene ana amatulukira pochokera m’chiberekero.+