Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Anthu asokonezeka.+ Nsautso ndi zowawa za pobereka zawagwera. Iwo akumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+ Akuyang’anana modabwa. Nkhope zawo zafiira ndi mantha.+

  • Yesaya 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 N’chifukwa chake m’chiuno mwanga mwadzaza ululu woopsa.+ Zopweteka zandigwira, ngati zowawa za mkazi amene akubereka.+ Ndazunguzika moti sindikumva. Ndasokonezeka moti sindikuona.

  • Yeremiya 49:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Taonani! Wina adzakwera kenako n’kutsika ngati chiwombankhanga chimene chikufuna kugwira chakudya chake.+ Adzatambasulira mapiko ake pa Bozira,+ ndipo pa tsikulo mtima wa amuna amphamvu a ku Edomu udzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.”+

  • Mika 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Tsopano n’chifukwa chiyani ukufuula kwambiri?+ Kodi mwa iwe mulibe mfumu, kapena kodi alangizi ako awonongedwa? Kodi n’chifukwa chake zowawa ngati za mkazi amene akubereka zakugwira?+

  • 1 Atesalonika 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena