Yeremiya 48:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Yehova wanena kuti, ‘Taonani! Monga mmene chiwombankhanga chimatsikira ndi kugwira chakudya chake,+ wina adzatambasula mapiko ake ndi kugwira Mowabu.+ Yeremiya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ine ndalumbira pa dzina langa+ kuti Bozira+ adzakhala chinthu chodabwitsa, chotonzedwa ndiponso malo owonongedwa.+ Iye adzakhala wotembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova.
40 “Yehova wanena kuti, ‘Taonani! Monga mmene chiwombankhanga chimatsikira ndi kugwira chakudya chake,+ wina adzatambasula mapiko ake ndi kugwira Mowabu.+
13 “Ine ndalumbira pa dzina langa+ kuti Bozira+ adzakhala chinthu chodabwitsa, chotonzedwa ndiponso malo owonongedwa.+ Iye adzakhala wotembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova.