Yeremiya 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Edomu adzakhala chinthu chodabwitsa.+ Aliyense wodutsa pafupi naye adzamuyang’anitsitsa modabwa ndi kumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yonse imene idzamugwera.+
17 “Edomu adzakhala chinthu chodabwitsa.+ Aliyense wodutsa pafupi naye adzamuyang’anitsitsa modabwa ndi kumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yonse imene idzamugwera.+