-
Zefaniya 2:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mzinda uwu unali wosangalala ndipo unkakhala mosaopa chilichonse.+ Mumtima mwake unali kunena kuti, ‘Ndilipo ndekha, ndipo palibe wondiposa.’+ Mzindawu wakhala chinthu chodabwitsa, malo amene nyama zakutchire zimagonamo momasuka. Aliyense wodutsa pafupi ndi mzindawu adzaimba mluzu ndipo adzapukusa mutu.”+
-