Yesaya 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwe unali mzinda wodzaza ndi chipwirikiti, waphokoso, komanso unali mudzi wokondwa.+ Anthu ako amene aphedwa, sanaphedwe ndi lupanga ndiponso sanaphedwe kunkhondo.+ Yesaya 47:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwe unali kunena kuti: “Ine ndidzakhala Dona mpaka kalekale,+ mpaka muyaya.” Sunaganizire zinthu izi mumtima mwako ndipo sunaganizire kuti zidzatha bwanji.+ Nahumu 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsoka mzinda wokhetsa magazi.+ Mzindawo wadzaza ndi chinyengo ndi chifwamba, moti nthawi zonse umafunkha zinthu za anthu ena.
2 Iwe unali mzinda wodzaza ndi chipwirikiti, waphokoso, komanso unali mudzi wokondwa.+ Anthu ako amene aphedwa, sanaphedwe ndi lupanga ndiponso sanaphedwe kunkhondo.+
7 Iwe unali kunena kuti: “Ine ndidzakhala Dona mpaka kalekale,+ mpaka muyaya.” Sunaganizire zinthu izi mumtima mwako ndipo sunaganizire kuti zidzatha bwanji.+
3 Tsoka mzinda wokhetsa magazi.+ Mzindawo wadzaza ndi chinyengo ndi chifwamba, moti nthawi zonse umafunkha zinthu za anthu ena.