Yesaya 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Panthaka ya anthu anga, pakungomera zitsamba zaminga.+ Zamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo. Zamera m’tauni imene kale inali yodzaza ndi chikondwerero.+ Amosi 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu mukumwera vinyo m’makapu akuluakulu+ ndipo mukudzola mafuta apamwamba kwambiri+ komanso simunamve ululu pamene tsoka linagwera Yosefe.+
13 Panthaka ya anthu anga, pakungomera zitsamba zaminga.+ Zamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo. Zamera m’tauni imene kale inali yodzaza ndi chikondwerero.+
6 Inu mukumwera vinyo m’makapu akuluakulu+ ndipo mukudzola mafuta apamwamba kwambiri+ komanso simunamve ululu pamene tsoka linagwera Yosefe.+