Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 22:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 n’kumuuza kuti: “Yehova wati, ‘Ndikulumbira+ pali dzina langa, kuti chifukwa cha zimene wachitazi, posakana kupereka mwana wako yekhayo,+

  • Yesaya 45:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndalumbira pa ine mwini.+ Mawuwo atuluka m’kamwa mwanga m’chilungamo,+ moti sadzabwerera.+ Ndalumbira kuti bondo lililonse lidzagwadira ine+ ndipo lilime lililonse lidzalumbira kwa ine,+

  • Amosi 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Yehova, Mulungu wa makamu, wanena kuti: ‘Ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndalumbira pa dzina langa kuti,+ “Ndikunyasidwa ndiponso ndikudana ndi kunyada kwa Yakobo+ ndi nsanja zake zokhalamo,+ chotero ndidzapereka mzindawu ndi zinthu zake zonse kwa adani ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena