Yeremiya 51:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova wa makamu walumbira m’dzina lake+ kuti, ‘M’dziko lako ndidzadzazamo amuna ngati dzombe+ ndipo amunawo adzaimba mokondwa chifukwa chokugonjetsa.’+ Amosi 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, walumbira mwa kuyera kwake+ kuti, ‘“Taonani! Masiku adzafika pamene mudzanyamulidwa ndi ngowe zokolera nyama ndipo otsala anu adzawakola ndi mbedza za nsomba.+ Aheberi 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.
14 Yehova wa makamu walumbira m’dzina lake+ kuti, ‘M’dziko lako ndidzadzazamo amuna ngati dzombe+ ndipo amunawo adzaimba mokondwa chifukwa chokugonjetsa.’+
2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, walumbira mwa kuyera kwake+ kuti, ‘“Taonani! Masiku adzafika pamene mudzanyamulidwa ndi ngowe zokolera nyama ndipo otsala anu adzawakola ndi mbedza za nsomba.+
13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.