-
Genesis 35:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Atanyamuka, Mulungu anachititsa kuti anthu amʼmizinda yowazungulira agwidwe ndi mantha, moti sanatsatire ana a Yakobo kuti amenyane nawo.
-