Genesis 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atatero anachoka, ndipo anthu a m’mizinda yowazungulira anagwidwa ndi mantha ochokera kwa Mulungu,+ moti sanatsatire ana a Yakobo kuti akawathire nkhondo.
5 Atatero anachoka, ndipo anthu a m’mizinda yowazungulira anagwidwa ndi mantha ochokera kwa Mulungu,+ moti sanatsatire ana a Yakobo kuti akawathire nkhondo.