Ekisodo 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Upange nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pansaluyi upetepo akerubi.+ Aheberi 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chiyembekezo+ chimene tili nachochi chili ngati nangula* wa miyoyo yathu ndipo n’chotsimikizika ndiponso chokhazikika. Chiyembekezo chimenechi chimatilowetsa mkati, kuseri kwa nsalu yotchinga,+ Aheberi 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+
31 “Upange nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pansaluyi upetepo akerubi.+
19 Chiyembekezo+ chimene tili nachochi chili ngati nangula* wa miyoyo yathu ndipo n’chotsimikizika ndiponso chokhazikika. Chiyembekezo chimenechi chimatilowetsa mkati, kuseri kwa nsalu yotchinga,+
20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+