Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni m’bale wako, kuti asamalowe konse m’malo oyera+ kuseri kwa nsalu yotchinga,+ patsogolo pa chivundikiro cha Likasa, kuopera kuti angafe,+ chifukwa ine ndidzaonekera mu mtambo+ pamwamba pa chivundikirocho.+

  • Levitiko 16:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Kenako iye azitenga chofukizira+ chodzaza ndi makala amoto ochokera paguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova. Azitenganso zofukiza zonunkhira zabwino kwambiri+ zokwana manja awiri+ odzaza, ndi kulowa nazo kuchipinda, kuseri kwa nsalu yotchinga.*+

  • Yohane 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiponso, ndikapita kukakukonzerani malo, ndidzabweranso+ kudzakutengerani kwathu,+ kuti kumene kuli ineko inunso mukakhale kumeneko.+

  • Aheberi 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma m’chipinda chachiwiricho, mkulu wa ansembe yekha ndiye anali kulowamo kamodzi pa chaka,+ ndipo sanali kulowamo popanda kutenga magazi.+ Magaziwo anali kuwapereka chifukwa cha iye mwini,+ komanso chifukwa cha machimo a anthu amene anachita mosadziwa.+

  • Aheberi 10:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena