Levitiko 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako iye azitenga chofukizira+ chodzaza ndi makala amoto ochokera paguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova. Azitenganso zofukiza zonunkhira zabwino kwambiri+ zokwana manja awiri odzaza nʼkulowa nazo kuchipinda, kuseri kwa katani.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2019, ptsa. 20-22 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 87
12 Kenako iye azitenga chofukizira+ chodzaza ndi makala amoto ochokera paguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova. Azitenganso zofukiza zonunkhira zabwino kwambiri+ zokwana manja awiri odzaza nʼkulowa nazo kuchipinda, kuseri kwa katani.+