Genesis 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anayang’ana kumunsi ku Sodomu ndi Gomora ndi kudera lonse la Chigawocho, ndipo anaona zoopsa. Kumeneko chiutsi chinali tolo! Chinali kufuka ngati chiutsi chochokera pa uvuni wa njerwa.+ Salimo 144:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, weramitsani kumwamba kuti mutsike.+Khudzani mapiri kuti afuke utsi.+
28 Ndiyeno anayang’ana kumunsi ku Sodomu ndi Gomora ndi kudera lonse la Chigawocho, ndipo anaona zoopsa. Kumeneko chiutsi chinali tolo! Chinali kufuka ngati chiutsi chochokera pa uvuni wa njerwa.+