Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+ Salimo 104:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Amayang’ana dziko lapansi ndipo limanjenjemera.+Amagwira mapiri ndipo amafuka utsi.+
18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+