Ekisodo 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo ndi kulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikiro,+ pakati pa akerubi awiriwo amene ali pamwamba pa likasa la umboni. Kuchokera pamenepo ndidzakulamula zonse zokhudza ana a Isiraeli.+ Salimo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anafika atakwera pakerubi wouluka.+Mulungu anali kuuluka mwaliwiro pamapiko a cholengedwa chauzimu.*+ Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+
22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo ndi kulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikiro,+ pakati pa akerubi awiriwo amene ali pamwamba pa likasa la umboni. Kuchokera pamenepo ndidzakulamula zonse zokhudza ana a Isiraeli.+
10 Iye anafika atakwera pakerubi wouluka.+Mulungu anali kuuluka mwaliwiro pamapiko a cholengedwa chauzimu.*+
80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+