-
Ezara 9:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Iwo anayamba kusonkhana kwa ine, aliyense akunjenjemera+ chifukwa cha mawu a Mulungu wa Isiraeli otsutsa kusakhulupirika kwa anthu amene anabwerera kuchokera ku ukapolo. Pa nthawiyi n’kuti ine nditakhala pansi ndili wokhumudwa ndi wachisoni kwambiri, ndipo ndinakhala choncho mpaka nthawi yopereka nsembe yambewu yamadzulo.+
-