Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano, bambo anga,+ onani. Taonani kansalu ka m’munsi mwa malaya anu akunja odula manja. Pakuti mmene ndinali kudula kansalu kameneka sindinakupheni. Ndiyetu dziwani ndi kuona kuti ndilibe maganizo oipa+ kapena oukira, ndipo sindinakuchimwireni, ngakhale kuti inuyo mukufunafuna moyo wanga kuti mundiphe.+

  • 1 Samueli 26:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Davideyo anawonjezera kuti: “N’chifukwa chiyani inu mbuyanga mukuthamangitsa ine mtumiki wanu?+ Ndachita chiyani ine, ndipo ndalakwa chiyani?+

  • Salimo 119:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  23 Akalonga asonkhana pamodzi kuti akambirane zondiukira.+

      Koma ine mtumiki wanu, ndimasinkhasinkha malangizo anu.+

  • Yohane 15:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Zili choncho kuti mawu olembedwa m’Chilamulo akwaniritsidwe. Mawu ake ndi akuti, ‘Anadana nane popanda chifukwa.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena