-
1 Samueli 24:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Tsopano, bambo anga,+ onani. Taonani kansalu ka m’munsi mwa malaya anu akunja odula manja. Pakuti mmene ndinali kudula kansalu kameneka sindinakupheni. Ndiyetu dziwani ndi kuona kuti ndilibe maganizo oipa+ kapena oukira, ndipo sindinakuchimwireni, ngakhale kuti inuyo mukufunafuna moyo wanga kuti mundiphe.+
-
-
Salimo 7:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Inu Yehova Mulungu wanga, ngati ndachita cholakwa chilichonse,+
Ngati manja anga achita zosalungama zilizonse,+
-
Yohane 10:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Yesu anawauza kuti: “Ndakuonetsani ntchito zambiri zabwino zochokera kwa Atate. Tsopano mukundiponya miyala chifukwa cha ntchito iti mwa zimenezi?”
-
-
Yohane 18:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Yesu anamuyankha kuti: “Ngati ndalankhula molakwika, pereka umboni wa cholakwikacho. Koma ngati ndalankhula moyenera, n’chifukwa chiyani ukundimenya?”
-
-
-