Yoswa 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Wamphamvu,+ Mulungu,+ Yehova,+ Wamphamvu, Mulungu, Yehova, iye akudziwa,+ ndipo nayenso Isiraeli adziwa.+ Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka+ ndiponso chifukwa cha kusakhulupirika pamaso pa Yehova,+ musatisiye amoyo lero. 2 Samueli 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wakubwezera mlandu wonse wa magazi a nyumba ya Sauli amene iwe unamulowa m’malo monga mfumu. Yehova wapereka ufumu m’manja mwa Abisalomu mwana wako. Ndipo tsopano tsoka lakugwera chifukwa uli ndi mlandu wamagazi!”+
22 “Wamphamvu,+ Mulungu,+ Yehova,+ Wamphamvu, Mulungu, Yehova, iye akudziwa,+ ndipo nayenso Isiraeli adziwa.+ Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka+ ndiponso chifukwa cha kusakhulupirika pamaso pa Yehova,+ musatisiye amoyo lero.
8 Yehova wakubwezera mlandu wonse wa magazi a nyumba ya Sauli amene iwe unamulowa m’malo monga mfumu. Yehova wapereka ufumu m’manja mwa Abisalomu mwana wako. Ndipo tsopano tsoka lakugwera chifukwa uli ndi mlandu wamagazi!”+