Salimo 50:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Wamphamvuyo,+ Yehova, Mulungu,+ walankhula+Ndipo akuitana dziko lapansi,+Kuchokera kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera.+ Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+
50 Wamphamvuyo,+ Yehova, Mulungu,+ walankhula+Ndipo akuitana dziko lapansi,+Kuchokera kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera.+
29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+