Yoswa 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Wamphamvu,+ Mulungu,+ Yehova,+ Wamphamvu, Mulungu, Yehova, iye akudziwa,+ ndipo nayenso Isiraeli adziwa.+ Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka+ ndiponso chifukwa cha kusakhulupirika pamaso pa Yehova,+ musatisiye amoyo lero. Yesaya 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kumbukirani zinthu zoyambirira zimene zinachitika kalekale,+ kuti ine ndine Mulungu+ ndipo palibenso Mulungu wina,+ kapena aliyense wofanana ndi ine.+ Yeremiya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+
22 “Wamphamvu,+ Mulungu,+ Yehova,+ Wamphamvu, Mulungu, Yehova, iye akudziwa,+ ndipo nayenso Isiraeli adziwa.+ Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka+ ndiponso chifukwa cha kusakhulupirika pamaso pa Yehova,+ musatisiye amoyo lero.
9 Kumbukirani zinthu zoyambirira zimene zinachitika kalekale,+ kuti ine ndine Mulungu+ ndipo palibenso Mulungu wina,+ kapena aliyense wofanana ndi ine.+
18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+