Deuteronomo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani masiku akale,+Ganizirani zaka za mibadwomibadwo ya m’mbuyomu.Funsa bambo ako ndipo akuuza,+Amuna achikulire pakati panu, ndipo akufotokozera.+ Yesaya 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Zinthu zoyamba zachitika,+ koma ndikukuuzani zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+
7 Kumbukirani masiku akale,+Ganizirani zaka za mibadwomibadwo ya m’mbuyomu.Funsa bambo ako ndipo akuuza,+Amuna achikulire pakati panu, ndipo akufotokozera.+
9 “Zinthu zoyamba zachitika,+ koma ndikukuuzani zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+