Deuteronomo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani masiku akale,Ganizirani zaka za mibadwo ya mʼmbuyo. Funsani bambo anu ndipo akuuzani,+Amuna achikulire pakati panu, ndipo akufotokozerani.
7 Kumbukirani masiku akale,Ganizirani zaka za mibadwo ya mʼmbuyo. Funsani bambo anu ndipo akuuzani,+Amuna achikulire pakati panu, ndipo akufotokozerani.