Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 18:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Davide pamodzi ndi asilikali ake ananyamuka, ndipo anakapha+ amuna 200 achifilisiti. Ndiyeno Davide anabwerako atatenga makungu awo a kunsonga,+ ndipo makungu onsewo anawapereka kwa mfumu kuti achite naye mgwirizano wa ukwati. Pamenepo Sauli anapereka Mikala, mwana wake wamkazi, kwa Davide kuti akhale mkazi wake.+

  • 1 Samueli 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ahimeleki anayankha mfumuyo kuti: “Ndani pakati pa atumiki anu onse ali ngati Davide,+ munthu wokhulupirika,+ mkamwini+ wa mfumu, mtsogoleri wa asilikali okulonderani ndiponso munthu wolemekezeka m’nyumba yanu?+

  • Miyambo 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyankha modekha kumabweza mkwiyo,+ koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+

  • Miyambo 25:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuleza mtima kumanyengerera mtsogoleri wa asilikali, ndipo lilime lofatsa likhoza kuthyola fupa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena