Genesis 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anawalamula kuti: “Mukafika kwa mbuyanga+ Esau, mukanene kuti, ‘Kapolo wanu Yakobo wanena kuti: “Ndinali kukhala ndi Labani monga mlendo, ndipo ndakhala kumeneko nthawi yaitali mpaka leroli.+ Miyambo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyankha modekha kumabweza mkwiyo,+ koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+
4 Anawalamula kuti: “Mukafika kwa mbuyanga+ Esau, mukanene kuti, ‘Kapolo wanu Yakobo wanena kuti: “Ndinali kukhala ndi Labani monga mlendo, ndipo ndakhala kumeneko nthawi yaitali mpaka leroli.+