Oweruza 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero iye anawayankha kuti: “Kodi ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?+ Kodi zokunkha za Efuraimu+ si zabwino kwambiri kuposa mphesa zimene Abi-ezeri+ wakolola? 1 Samueli 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kulingalira bwino kwako.+ Udalitsike chifukwa cha kundigwira lero kuti ndisapalamule mlandu wamagazi+ ndi kudzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.+ Miyambo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuleza mtima kumanyengerera mtsogoleri wa asilikali, ndipo lilime lofatsa likhoza kuthyola fupa.+
2 Chotero iye anawayankha kuti: “Kodi ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?+ Kodi zokunkha za Efuraimu+ si zabwino kwambiri kuposa mphesa zimene Abi-ezeri+ wakolola?
33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kulingalira bwino kwako.+ Udalitsike chifukwa cha kundigwira lero kuti ndisapalamule mlandu wamagazi+ ndi kudzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.+