1 Samueli 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho musalole kuti zimenezi zikhale zokuvutitsani chikumbumtima ndi zokhumudwitsa mumtima mwanu mbuyanga, mwa kukhetsa magazi popanda chifukwa+ ndi kudzipulumutsa nokha ndi dzanja lanu.+ Mukatero, Yehova adzakuchitirani zabwino mbuyanga, ndipo mudzandikumbukire+ ine kapolo wanu wamkazi.” Salimo 56:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+ Aroma 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+
31 Choncho musalole kuti zimenezi zikhale zokuvutitsani chikumbumtima ndi zokhumudwitsa mumtima mwanu mbuyanga, mwa kukhetsa magazi popanda chifukwa+ ndi kudzipulumutsa nokha ndi dzanja lanu.+ Mukatero, Yehova adzakuchitirani zabwino mbuyanga, ndipo mudzandikumbukire+ ine kapolo wanu wamkazi.”
13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+
19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+