Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+ 1 Samueli 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzandiweruzira mlanduwu+ ndi kuchitapo kanthu kuti andimasule m’manja mwanu.” Salimo 94:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Inu Yehova, Mulungu wobwezera anthu oipa,+Inu Mulungu wobwezera anthu oipa, walani!+ Aroma 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+
15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzandiweruzira mlanduwu+ ndi kuchitapo kanthu kuti andimasule m’manja mwanu.”
19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+