Salimo 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Weruzani mlandu wanga inu Yehova, motsutsana ndi adani anga.+Menyani nkhondo ndi kugonjetsa amene akumenyana ndi ine.+ Salimo 43:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+ Salimo 119:154 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 154 Ndiyankhireni mlandu wanga ndi kundipulumutsa.+Ndisungeni wamoyo mogwirizana ndi mawu anu.+ Mika 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkwiyo waukulu wa Yehova ndiupirira chifukwa ndamuchimwira.+ Ndiupirirabe kufikira ataweruza mlandu wanga mondikomera ndi kundichitira chilungamo.+ Iye adzandipititsa pamalo owala ndipo ndidzaona kulungama kwake.+
35 Weruzani mlandu wanga inu Yehova, motsutsana ndi adani anga.+Menyani nkhondo ndi kugonjetsa amene akumenyana ndi ine.+
43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+
9 Mkwiyo waukulu wa Yehova ndiupirira chifukwa ndamuchimwira.+ Ndiupirirabe kufikira ataweruza mlandu wanga mondikomera ndi kundichitira chilungamo.+ Iye adzandipititsa pamalo owala ndipo ndidzaona kulungama kwake.+