Maliro 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndapandukira+ mawu a pakamwa pake.Anthu nonsenu, tamverani mawu anga, ndipo muone ululu umene ndikumva.Anamwali anga ndi anyamata anga atengedwa kupita ku ukapolo.+ Luka 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Basi ndinyamuka ndizipita+ kwa bambo anga ndikawauze kuti: “Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+
18 Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndapandukira+ mawu a pakamwa pake.Anthu nonsenu, tamverani mawu anga, ndipo muone ululu umene ndikumva.Anamwali anga ndi anyamata anga atengedwa kupita ku ukapolo.+
18 Basi ndinyamuka ndizipita+ kwa bambo anga ndikawauze kuti: “Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+