Ekisodo 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anali kugulula mawilo a magaleta awo moti anali kuwayendetsa movutikira.+ Pamenepo Aiguputo anayamba kunena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+ Yoswa 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Yoswa anagwira mafumu onsewa n’kulanda malo awo pa nthawi imodzi,+ chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndiye anali kuwamenyera nkhondo.+ Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+
25 Iye anali kugulula mawilo a magaleta awo moti anali kuwayendetsa movutikira.+ Pamenepo Aiguputo anayamba kunena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+
42 Yoswa anagwira mafumu onsewa n’kulanda malo awo pa nthawi imodzi,+ chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndiye anali kuwamenyera nkhondo.+
7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+