Ekisodo 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzakumenyerani nkhondo,+ ndipo inu mudzakhala chete, osachitapo kalikonse.” Deuteronomo 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova Mulungu wanu ndiye akukutsogolerani. Adzakumenyerani nkhondo+ mofanana ndi zonse zimene anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona,+ Deuteronomo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amuna inu, musawaope amenewo, chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo.’+
30 Yehova Mulungu wanu ndiye akukutsogolerani. Adzakumenyerani nkhondo+ mofanana ndi zonse zimene anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona,+